Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

GAWO 6 • MACHITIDWE 15:36–18:22

“Tiyeni Tibwerere . . . Kuti Tikachezere Abale”

“Tiyeni Tibwerere . . . Kuti Tikachezere Abale”

MACHITIDWE 15:36

Kodi oyang’anira madera amagwira ntchito yofunika iti mumpingo wa Chikhristu? Kodi timapeza madalitso otani tikavomera ndi mtima wonse kugwira ntchito imene gulu la Mulungu latipatsa? Kodi tingafotokoze bwanji mfundo za m’Malemba mogwira mtima, nanga n’chifukwa chiyani tiyenera kusintha uthenga umene tikulalikira kuti ugwirizane ndi anthu omwe tikuwalalikirawo? Tipeza mayankho a mafunso amenewa pamene tikuyendera limodzi ndi Paulo pa ulendo wake wachiwiri waumishonale.