Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

GAWO 1 • MACHITIDWE 1:1–6:7

“Mwadzaza Yerusalemu Yense ndi Mfundo Zimene Mukuphunzitsa”

“Mwadzaza Yerusalemu Yense ndi Mfundo Zimene Mukuphunzitsa”

MACHITIDWE 5:28

Kungoyambira pamene ophunzira a Yesu analandira mzimu woyera pa Pentekosite mu 33 C.E., iwo anayamba kugwira mwakhama ntchito yochitira umboni za Ufumu wa Mulungu. M’gawoli, tikambirana nkhani yosangalatsa yonena za mmene mpingo wa Chikhristu unayambira, ntchito yaikulu yolalikira imene inachitika ku Yerusalemu komanso mmene atumwi anasonyezera kulimba mtima pamene adani awo anapitiriza kuwatsutsa kwambiri.