Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

BOKOSI 11A

Alonda Ena Achitsanzo Chabwino

Alonda Ena Achitsanzo Chabwino

Alondawo ankatsutsidwa koma anakhalabe okhulupirika ndipo ankalengeza uthenga wochenjeza komanso wabwino.

ISIRAELI WAKALE

  • Yesaya 778–cha m’ma 732 B.C.E.

  • Yeremiya 647-580 B.C.E.

  • Ezekieli 613–cha m’ma 591 B.C.E.

NTHAWI YA ATUMWI

  • Yohane M’batizi 29-32 C.E.

  • Yesu 29-33 C.E.

  • Paulo cha m’ma 34–cha m’ma 65 C.E.

MASIKU ANO

  • C. T. Russell ndi anzake cha m’ma 1879-1919

  • Kapolo Wokhulupirika 1919–Mpaka lero