Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

BOKOSI 5A

“Iwe Mwana wa Munthu, Kodi Waona Zimenezi?”

“Iwe Mwana wa Munthu, Kodi Waona Zimenezi?”

Zinthu 4 zonyansa kwambiri zimene Ezekieli anaona m’bwalo la mkati la kachisi. (Ezek. 8:5-16)

1. FANO LOIMIRA NSANJE

2. AKULUAKULU 70 AKUPEREKA NSEMBE ZOFUKIZA KWA MILUNGU YABODZA

3. ‘AZIMAYI AKULIRIRA MULUNGU WOTCHEDWA TAMUZI’

4. AMUNA 25 ‘AKUGWADIRA DZUWA’