Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

BOKOSI 10A

Kulambira Koyera—Kunabwezeretsedwa Pang’onopang’ono

Kulambira Koyera—Kunabwezeretsedwa Pang’onopang’ono
  • “Gobedegobede”

    William Tyndale ndi anzake anamasulira Baibulo m’Chingelezi komanso m’zilankhulo zina

  • “Mitsempha ndi mnofu”

    Charles T. Russell ndi anzake anabwezeretsa choonadi cha m’Baibulo

  • “Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira”

    Anthu a Yehova ‘atakhala ndi moyo’ mu 1919, anayamba kugwira ntchito yolalikira mwakhama