Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

BOKOSI 12A

Kuphatikiza Ndodo Ziwiri

Kuphatikiza Ndodo Ziwiri

Yehova anauza Ezekieli kuti alembe pa ndodo imodzi kuti “ndodo ya Yuda” komanso pa ndodo ina alembe kuti “ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu.”

“ndodo ya Yuda”

KALE

Ufumu wa Yuda wa mafuko awiri

MASIKU ANO

Odzozedwa

“ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu”

KALE

Ufumu wa Isiraeli wa mafuko 10

MASIKU ANO

Nkhosa zina

“zikhale ndodo imodzi mʼdzanja lako”

KALE

537 B.C.E. Anthu amene ankalambira Mulungu woona anabwera kuchokera m’mitundu yosiyanasiyana, anamanganso Yerusalemu ndipo anayamba kulambira Yehova monga mtundu umodzi.

MASIKU ANO

Kuyambira mu 1919, anthu a Mulungu pang’ono ndi pang’ono akugwirizananso kuti azitumikira Mulungu ngati “gulu limodzi.”