BOKOSI 8B
Maulosi Atatu Okhudza Mesiya
1. “Amene Ali Woyenerera Mwalamulo” (Ezekieli 21:25-27)
NTHAWI ZA ANTHU AKUNJA (607 B.C.E.–1914 C.E.)
-
607 B.C.E.—Zedekiya anachotsedwa pa ufumu
-
1914 C.E.—Yesu amene ndi “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu komanso Mesiya anaikidwa kukhala Mfumu ndipo anakhala M’busa ndiponso Wolamulira
Ezekieli 34:22-24)
2. “Mtumiki Wanga . . . Adzawadyetsa Komanso Adzakhala M’busa Wawo” (MASIKU OTSIRIZA (1914 C.E.–PAMBUYO PA ARAMAGEDO)
-
1914 C.E.—Yesu amene ndi “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu komanso Mesiya anaikidwa kukhala Mfumu ndipo anakhala M’busa ndiponso Wolamulira
-
1919 C.E.—Kapolo wokhulupirika komanso wanzeru anasankhidwa kuti aziweta nkhosa za Mulungu
Akhristu odzozedwa okhulupirika anasonkhanitsidwa pamodzi ndi Mesiya yemwenso ndi Mfumu, ndipo kenako anakhala gulu limodzi ndi a khamu lalikulu
-
PAMBUYO PA ARAMAGEDO—Madalitso amene adzakhalepo Mfumu ikamadzalamulira adzakhalapo mpaka kalekale
3. “Onsewo Adzalamuliridwa ndi Mfumu Imodzi” Mpaka Kalekale (Ezekieli 37:22, 24-28)
MASIKU OTSIRIZA (1914 C.E.–PAMBUYO PA ARAMAGEDO)