Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

BOKOSI 8A

Ulosi Wokhudza Mesiya​—Mtengo Waukulu Wamkungudza

Ulosi Wokhudza Mesiya​—Mtengo Waukulu Wamkungudza

EZEKIELI 17:3-24

  • 1. Nebukadinezara anatenga Yehoyakini n’kupita naye ku Babulo

  • 2. Nebukadinezara anasankha Zedekiya kukhala mfumu ku Yerusalemu

  • 3. Zedekiya anapandukira Yehova ndipo anapita ku Iguputo kukapempha kuti amuthandize pa nkhondo

  • 4. Yehova anaika Mwana wake pa Phiri la Ziyoni wakumwamba

  • 5. Yesu akamadzalamulira monga mfumu, anthu omvera azidzakhala motetezeka