Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Ziwerengero Zonse za 2018

Ziwerengero Zonse za 2018
  • Nthambi za Mboni za Yehova: 87

  • Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 240

  • Mipingo Yonse: 119,954

  • Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 20,329,317

  • Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 19,521

  • Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira *: 8,579,909

  • Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,360,594

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2017: 1.4

  • Obatizidwa Onse *: 281,744

  • Avereji ya Apainiya * Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,267,808

  • Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 446,642

  • Maola Onse Amene Tinalalikira: 2,074,655,497

  • Avereji ya Maphunziro a Baibulo * Mwezi Uliwonse: 10,079,709

M’chaka cha utumiki cha 2018, * a Mboni za Yehova anagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 214 miliyoni a ku America posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira dera pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 20,331 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko Lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

^ ndime 7 Wofalitsa ndi munthu amene amalalikira mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengerochi, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

^ ndime 10 Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?

^ ndime 11 Mpainiya ndi wa Mboni wachitsanzo chabwino amene amadzipereka kuti azilalikira uthenga wabwino kwa maola enaake mwezi uliwonse.

^ ndime 14 Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Phunziro la Baibulo N’chiyani?

^ ndime 15 Chaka chautumiki cha 2018 chinayamba pa September 1, 2017, ndipo chinatha pa August 31, 2018.