Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Ziwerengero Zonse za 2020

Ziwerengero Zonse za 2020
  • Nthambi za Mboni za Yehova: 87

  • Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 240

  • Mipingo Yonse: 120,387

  • Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 17,844,773

  • Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 21,182

  • Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira *: 8,695,808

  • Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,424,185

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2019: -0.6

  • Obatizidwa Onse *: 241,994

  • Avereji ya Apainiya * Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,299,619

  • Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 338,568

  • Maola Onse Amene Tinalalikira: 1,669,901,531

  • Avereji ya Maphunziro a Baibulo * Mwezi Uliwonse: 7,705,765

M’chaka chautumiki cha 2020, * a Mboni za Yehova anagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 231 miliyoni posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira dera pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 20,994 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko Lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

^ ndime 7 Wofalitsa ndi munthu amene amalalikira mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengerochi, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

^ ndime 10 Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?

^ ndime 11 Mpainiya ndi wa Mboni wachitsanzo chabwino amene amadzipereka kuti azilalikira uthenga wabwino kwa maola enaake mwezi uliwonse.

^ ndime 14 Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Phunziro la Baibulo N’chiyani?

^ ndime 15 Chaka chautumiki cha 2020 chinayamba pa 1 September, 2019, ndipo chinatha pa 31 August, 2020.