Chinyengo YAMBANI Chinyengo 2Ak 6:4, 6; Yak 3:17 Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni: Mt 23:7, 23-28—Yesu anadzudzula atsogoleri achipembedzo chifukwa cha zochita zawo zachinyengo Aga 2:11-14—Mtumwi Paulo anadzudzula mtumwi Petulo chifukwa chochita zachiphamaso Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi NSANJA YA OLONDA Kodi Anthu Adzasiya Kuchita Zachinyengo? Kodi munasiya ndale, chipembedzo kapena bizinezi inayake mutakhumudwa chifukwa cha chinyengo? YESU—NDI NJIRA, CHOONADI NDI MOYO Tsiku Lomaliza Limene Yesu Anapezeka pa Kachisi Anawaphunzitsa mfundo yofunika kwambiri pogwiritsa ntchito chitsanzo cha mkazi wamasiye wosauka. ZOKHUDZA IFEYO Pemphani Kuti Tidzakuyendereni Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Chinyengo MALEMBA OTHANDIZA PA MOYO WA CHIKHRISTU Chinyengo Chichewa Chinyengo https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/d8f8c0370e/images/syn_placeholder_sqr.png scl p. 23