Kudzitama
Sl 94:4; 1Ak 13:4; Yak 3:5, 14
Onaninso Miy 21:24; Yer 9:23, 24
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Owe 7:1-7—Yehova anachepetsa asilikali a Gidiyoni kuti atsale 300 n’cholinga chofuna kumuthandiza kudziwa kuti Yehova ndi amene adzachititse kuti apambane nkhondoyo.
2Mf 18:28-35—Senakeribu Mfumu ya Asuri, inagwiritsa ntchito nthumwi yake polankhula modzitama kuti Yehova sangapulumutse Yerusalemu m’manja mwa Asuri