Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kukhulupirika

Kukhulupirika

Sl 18:25; Lu 1:74, 75; Aef 4:24; Chv 15:4

Onaninso Sl 116:15; 145:17

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ru 1:16, 17; 3:10​—Rute anatsimikiza mtima kuti akhalabe wokhulupirika kwa Naomi komanso kwa Yehova

    • 2Mf 2:1, 2, 4, 6​—Elisa anatsimikiza mtima kuti akhala wokhulupirika kwa mneneri Eliya