Kukhulupirira Yehova
Miy 3:5, 21-26; Yes 26:3, 4; Yer 17:7, 8
Onaninso Sl 34:8; 40:4, 5; Miy 20:22; Yes 30:15
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
1Mb 5:18-20, 22—Mitundu ina ya ana a Isiraeli inagonjetsa adani awo chifukwa chokhulupirira Yehova
2Mb 14:9-13—Mfumu Asa anapemphera kwa Yehova komanso anasonyeza kuti anali chikhulupiriro cholimba kuti Yehova amuthandiza pa nthawi imene ankaopsezedwa ndi adani