Kulimba Mtima
Onaninso Sl 27:1, 2, 13, 14; Mac 28:15; Afi 1:14
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Yos 1:1-3, 8, 9—Yehova analamula Yoswa kuti akhale wolimba mtima n’cholinga choti akwanitse utumiki womwe anamupatsa
Mac 16:12, 22-24; 17:1, 2; 1At 2:2 —Mtumwi Paulo anapitiriza kulalikira molimba mtima ngakhale kuti ankazunzidwa kwambiri