Kuona Mtima
De 25:13-16; 2Ak 8:21; Aef 4:25; Ahe 13:18
Onaninso Yob 6:25; Miy 3:32; 6:16-19; 2Ak 6:3, 4, 7, 8
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Sl 15:1-5—Yehova anafotokoza zinthu zomwe anthu amene angakhale anzake ayenera kuchita ndipo chimodzi mwa zinthuzi ndi kukhala oona mtima
Mac 5:1-10—Hananiya ndi Safira anaphedwa chifukwa chosachita zinthu moona mtima