Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kupanda Ulemu

Kupanda Ulemu

Kodi tiyenera kupewa kuchita zinthu ziti zosonyeza kupanda ulemu?

Sl 10:13; 3Yo 9, 10

Onaninso Sl 74:10, 18; Yuda 8, 10

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Sa 2:12-17, 22-25, 27-30​—Ana aamuna a Mkulu wa Ansembe Eli sankalemekeza dongosolo la Yehova lokhudza kulambira ndipo Eli analephera kuwalangiza. Zimenezi zinasonyeza kuti Eli nayenso sanalemekeze Yehova

    • 2Mf 1:9-15​—Yehova anapha asilikali omwe sanalemekeze mneneri wake Eliya koma sanaphe amene anali odzichepetsa