Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Makhalidwe Oipa

Makhalidwe Oipa

Kodi Akhristu ayenera kupewa kuchita zinthu zoipa ziti?

Mawu achipongwe

Mt 5:22; 1Ak 6:9, 10; Aef 4:31

Onaninso Eks 22:28; Mla 10:20; Yuda 8

Kulandira kapena kupereka ziphuphu

Eks 23:8; Sl 26:9, 10; Miy 17:23

Onaninso De 10:17; 16:19; Sl 15:1, 5

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Sa 8:1-5​—Ana a mneneri Samueli ankalandira ziphuphu komanso kupotoza chilungamo m’malo motengera chitsanzo chabwino cha bambo awo

    • Ne 6:10-13​—Adani a anthu a Yehova analipira mneneri wonyenga dzina lake Semaya kuti aopseze Bwanamkubwa Nehemiya komanso kubwezeretsa m’mbuyo ntchito ya Yehova

Kudzitama

Onani “Kudzitama

Khalidwe lopanda manyazi; khalidwe lonyansa; chiwerewere; chigololo

Onani “Chiwerewere

Mpikisano; Kupikisana

Mla 4:4; Aga 5:26

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mko 9:33-37; 10:35-45​—Yesu anadzudzula atumwi ake mobwerezabwereza chifukwa cha khalidwe lawo lokonda mpikisano kuti apatsidwe maudindo

    • 3Yo 9, 10​—Diotirefe ankakonda “kukhala woyamba” pakati pa abale

Kuyambitsa magawano; kulimbikitsa magulu ampatuko

Kuledzera; kumwa mopitirira malire

Miy 20:1; 23:20, 29-35; 1Ak 5:11; 6:9, 10

Onaninso Aef 5:18; 1Ti 3:8; Tit 2:3; 1Pe 4:3

Onaninso “Kumwa mowa

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 9:20-25​—Nowa analedzera ndipo zimenezi zinachititsa kuti Hamu ndi mwana wake Kanani achite tchimo lalikulu

    • Da 5:1-6, 30​—Mfumu Belisazara ataledzera, ananyoza Yehova ndipo zotsatirapo zake anaphedwa komanso ufumu wake unatha

Kulanda

Sl 62:10; 1Ak 5:10, 11; 6:9, 10

Onaninso Miy 1:19; 15:27

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Yer 22:11-17​—Yehova anadzudzula Mfumu Salumu (Yehoahazi) chifukwa cha kuba mwachinyengo, kulanda zinthu za ena ndi machimo ena akuluakulu

    • Lu 19:2, 8​—Zakeyu, yemwe anali mkulu wa okhometsa misonkho, analapa machimo ake oba zinthu mwachinyengo ndipo analonjeza kuti abweza chilichonse chimene analanda

    • Mac 24:26, 27​—Bwanamkubwa Felike ankaganiza kuti Mtumwi Paulo amupatsa chiphuphu koma sanatero

Chiphamaso kapena kudzionetsera

Yob 32:21, 22; Sl 5:9; 12:2, 3; Miy 26:24-28; 29:5

Onaninso Miy 28:23; 1At 2:3-6

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Lu 18:18, 19​—Yesu anakana kuchita zinthu modzionetsera

    • Mac 12:21-23​—Mfumu Herode Agiripa analolera kuti anthu azimutamanda ngati mulungu; anaphedwa chifukwa chosalemekeza Mulungu

Dyera

Miseche; kulowerera nkhani za eni

Kulambira mafano

Onani “Kulambira mafano

Kunama; kunena bodza

Onani “Kunama

Kunama; kuneneza

Onani “Kunama

Kugwiritsa ntchito magazi molakwika

Ge 9:4; De 12:16, 23; Mac 15:28, 29

Onaninso Le 3:17; 7:26

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Sa 14:32-34​—Aisiraeli anachimwira Yehova podya nyama asanakhetse magazi ake

Kupha

Eks 20:13; Mt 15:19; 1Pe 4:15

Onaninso Mt 5:21, 22; Mko 7:21

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 4:4-16​—Ngakhale kuti Yehova anapereka malangizo achikondi kwa Kaini, koma iye anapha m’bale wake Abele yemwe anali wolungama

    • 1Mf 21:1-26; 2Mf 9:26​—Dyera linachititsa kuti Mfumu yoipa Ahabu komanso Mfumukazi Yezebeli akonze zoti Naboti ndi ana ake aamuna aphedwe

Kung’ung’udza

1Ak 10:10; Afi 2:14; Yuda 16

Onaninso Nu 11:1

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Nu 14:1-11, 26-30​—Pamene Aisiraeli anayamba kung’ung’udzira Mose ndi Aroni, Yehova anaona kuti akung’ung’udzira Iyeyo

    • Yoh 6:41-69​—Ayuda ankang’ung’udza za Yesu; ophunzira ake ena anamusiya

Nthabwala zotukwana

Zolaula

Onani “Zolaula

Kukangana

Kukangana

Kunyoza

Miy 19:29; 24:9

Onaninso Miy 17:5; 22:10; 2Pe 3:3, 4

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 2Mb 36:15-21​—Anthu a Mulungu opanduka analangidwa koopsa chifukwa chonyoza atumiki komanso aneneri a Mulungu

    • Yob 12:4; 17:2; 21:3; 34:7​—Yobu yemwe anali munthu wolungama ananyozedwa pa nthawi yomwe ankakumana ndi mayesero ovuta

Kuba

Onani “Kuba

Mikangano; chiwawa

Sl 11:5; Miy 3:31; 29:22

Onaninso 1Ti 3:2, 3; Tit 1:7

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Eks 21:22-27​—Chilamulo cha Mose chinkanena kuti munthu akamachita zachiwawa ndi kuvulaza kapena kupha mnzake, azipatsidwa chilango

Kuopseza

Aef 6:9; 1Pe 2:23

Onaninso Sl 10:4, 7; 73:3, 8

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mac 4:15-21​—Khoti la Sanihedirini linaopseza ophunzira a Yesu pofuna kuti asiye kugwira ntchito yolalikira

Maphwando aphokoso

Aro 13:13; Aga 5:19, 21; 1Pe 4:3

Onaninso Miy 20:1; 1Ak 10:31

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Da 5:1-4, 30​—Pa “phwando lalikulu” limene Mfumu Belisazara inakonza, anthu anamwa mowa wambiri ndiponso sanalemekeze Yehova zomwe zinachititsa kuti Mfumuyi iphedwe