Makolo a Mwamuna Kapena Mkazi wanu
N’chifukwa chiyani makolo sayenera kulowelera za m’banja la mwana wawo?
Onaninso Sl 34:14; Mt 5:9; Aro 12:18; 14:10-13
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Eks 18:1-27—Mneneri Mose ankalemekezana kwambiri ndi apongozi ake, a Yetero