Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Malangizo

Malangizo

N’chifukwa chiyani tiyenera kugwiritsa ntchito Baibulo popereka malangizo?

N’chifukwa chiyani tonsefe timafunikira kupatsidwa malangizo?

Kodi malangizo amene Yehova amatipatsa ndi umboni wa chiyani?

Miy 3:11, 12; Ahe 12:7-9

Onaninso De 8:5; Miy 13:24; Chv 3:19

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 2Sa 12:9-13; 1Mf 15:5; Mac 13:22​—Ngakhale kuti Mfumu Davide anachita machimo akuluakulu, Yehova anamupatsa malangizo mwachikondi ndipo anamukhululukira

    • Yon 1:1-4, 15-17; 3:1-3​—Yona atathawa utumiki womwe anapatsidwa, Yehova anamupatsa malangizo kenako anamulola kuti apitenso

N’chifukwa chiyani ndi nzeru kutsatira malangizo omwe Mulungu amatipatsa?

Kodi amene amakana kutsatira malangizo ochokera kwa Mulungu adzakumana ndi zotani?

Miy 1:24-26; 13:18; 15:32; 29:1

Onaninso Yer 7:27, 28, 32-34

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Yer 5:3-7​—Anthu a Mulungu anaumitsa mitima yawo n’kukana kusintha atapatsidwa malangizo, choncho anapatsidwa chilango champhamvu

    • Zef 3:1-8​—Anthu okhala ku Yerusalemu anakumana ndi mavuto aakulu chifukwa chokana kutsatira malangizo a Yehova

Kodi timapindula bwanji tikamamvera malangizo a Yehova?

Miy 4:13; 1Ak 11:32; Tit 1:13; Ahe 12:10, 11

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • De 30:1-6​—Mneneri Mose anauza Aisiraeli kuti akamvera malangizo a Yehova adzalandira madalitso

    • 2Mb 7:13, 14​—Yehova anauza Mfumu Solomo kuti ngati anthu angamvere malangizo ake, iye adzawachitira zinthu zabwino

N’chifukwa chiyani ndi bwino kuphunzirapo kanthu pa malangizo amene anthu ena apatsidwa?

N’chifukwa chiyani sitiyenera kusangalala ngati anthu ena apatsidwa chilango?

Kodi tiyenera kuchita chiyani kuti tizipindula ndi malangizo komanso chilango chochokera kwa Mulungu?

Yos 1:8; Yak 1:25

Onaninso De 17:18, 19; Sl 119:97

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 1Mb 22:11-13​—Mfumu Davide analonjeza mwana wake Solomo kuti Yehova adzamudalitsa ngati adzatsatira malangizo ake mosamala

    • Sl 1:1-6​—Yehova analonjeza kuti adzadalitsa anthu amene amawerenga ndi kuganizira mozama chilamulo chake

N’chifukwa chiyani makolo achikondi amapereka malangizo kwa ana awo?

Onani “Makolo

Kodi ana ayenera kuchita chiyani makolo awo akamawapatsa malangizo?