Mtendere
Kodi timadziwa bwanji kuti Yehova amaona kuti mtendere ndi wofunika kwambiri?
Kodi tingatani kuti tikhale amtendere komanso kuti tizikhala mwamtendere ndi anthu ena?
Sl 119:165; Yes 48:17, 18; Aro 12:17-21; Afi 4:6-9
Onaninso Yoh 16:33; Aef 6:14, 15; Akl 3:15
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Ge 32:9-21; 33:1-4—Yakobo anachita zambiri kuti akhazikitse mtendere ndi m’bale wake Esau
Mt 5:23-26—Yesu anafotokoza ubwino wokhala mwamtendere komanso chifukwa chake tifunika kumakhala mwamtendere ndi anthu ena