Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zolaula

Zolaula

Yob 31:1; Sl 101:2, 3; Mt 5:27-30; Akl 3:5

Onaninso 1Ak 6:18; Aef 4:17-19

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 6:1, 2; Yuda 6​—Angelo ena anayang’ana azimayi mowasirira, kenako anachita machimo aakulu n’kuwononga ubwenzi wawo ndi Yehova

    • 2Sa 11:2-4​—Mfumu Davide ankayang’anitsitsa Bati-seba ali kubafa akusamba, zomwe zinachititsa kuti achite tchimo la chigololo komanso kupha mwamuna wake