Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

GAWO 1

Kuwala Kwenikweni kwa Dziko

Kuwala Kwenikweni kwa Dziko

Pachiyambi, Mawu anali ndi Mulungu ndipo Mawuyo anali mulungu (gnj 1 00:00–00:43)

Mulungu anagwiritsa ntchito Mawuyo kulenga zinthu zina zonse (gnj 1 00:44–01:00)

Moyo ndiponso kuwala zinakhalapo kudzera mwa Mawuyo (gnj 1 01:01–02:11)

Mdimawo sunagonjetse kuwalako (gnj 1 02:12–03:59)

Luka akufotokoza mmene zinthu zinalili komanso chifukwa chake akulemba nkhaniyi, akulembera a Teofilo (gnj 1 04:13–06:02)

Gabirieli ananeneratu za kubadwa kwa Yohane M’batizi (gnj 1 06:04–13:53)

Gabirieli ananeneratu za kubadwa kwa Yesu (gnj 1 13:52–18:26)

Mariya wapita kwa Elizabeti, wachibale wake (gnj 1 18:27–21:15)

Mariya analemekeza Yehova (gnj 1 21:14–24:00)

Kubadwa kwa Yohane komanso kumupatsa dzina (gnj 1 24:01–27:17)

Ulosi wa Zekariya (gnj 1 27:15–30:56)

Mariya anakhala woyembekezera kudzera mwa mzimu woyera; zimene Yosefe anachita (gnj 1 30:58–35:29)

Yosefe ndi Mariya anapita ku Betelehemu; kubadwa kwa Yesu (gnj 1 35:30–39:53)

Angelo anaonekera kwa abusa ali kutchire (gnj 1 39:54–41:40)

Abusa anapita kukhola la ng’ombe (gnj 1 41:41–43:53)

Yesu anakamupereka kwa Yehova kukachisi (gnj 1 43:56–45:02)

Simiyoni anali ndi mwayi woona Khristu (gnj 1 45:04–48:50)

Anna analankhula zokhudza mwanayo (gnj 1 48:52–50:21)

Okhulupirira nyenyezi anafika komanso Herode anakonza zoti ana aphedwe (gnj 1 50:25–55:52)

Yosefe anatenga Mariya ndi Yesu n’kuthawira ku Iguputo (gnj 1 55:53–57:34)

Herode anapha ana onse aamuna ku Betelehemu komanso m’zigawo zake zonse (gnj 1 57:35–59:32)

Banja la Yesu linakhazikika ku Nazareti (gnj 1 59:34–1:03:55)

Zimene Yesu anachita kukachisi ali ndi zaka 12 (gnj 1 1:04:00–1:09:40)

Yesu anabwerera ku Nazareti ndi makolo ake (gnj 1 1:09:41–1:10:27)

Kuwala kwenikweni kunali kutatsala pang’ono kubwera m’dziko (gnj 1 1:10:28–1:10:55)