Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Muzichita Zinthu Mwamphamvu

Muzichita Zinthu Mwamphamvu

YOSWA 1:9

M’MAWA

  • 9:40 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:50 Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero

  • 10:00 Yehova Ndi Amene Amatipatsa Mphamvu

  • 10:15 Muzichita Zinthu Mwamphamvu Polimbitsa Chikhulupiriro Chanu

  • 10:30 Muzichita Zinthu Mwamphamvu Polalikira ndi Kuphunzitsa Ena

  • 10:55 Nyimbo Na. 7 ndi Zilengezo

  • 11:05 Yehova Amatipatsa Mphamvu Tikafooka

  • 11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:05 Nyimbo Na. 79

MASANA

  • 1:20 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:30 Nyimbo Na. 102

  • 1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu

  • 1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:15 Nkhani Yosiyirana: Muzichita Zinthu Mwamphamvu Posonyeza Kuti Muli Kumbali ya Yehova

    • Achinyamata

    • Anthu a pa Banja

  • 2:45 Nyimbo Na. 126 ndi Zilengezo

  • 2:55 “Limbani M’chikhulupiriro, . . . Khalani Amphamvu”

  • 3:55 Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero