Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. N’chifukwa chiyani sitiyenera kukayikira kuti Yehova atilimbitsa mtima tikamupempha? (Sal. 138:3)

  2. Kodi tingatani kuti tikhale olimba mtima ngati atumiki a Mulungu akale? (Mac. 4:31)

  3. Kodi tingalimbe bwanji mtima mu utumiki? (1 Ates. 2:2)

  4. N’chiyani chimatithandiza kukhala olimba mtima tikamakumana ndi mavuto? (1 Pet. 2:21-23)

  5. Kodi Akhristu olimba mtima adzalandira mphoto iti? (Aheb. 10:35)