Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. Kodi tingasonyeze bwanji kuti timakonda Mulungu? (Deut. 13:3, 4; 1 Yoh. 5:3)

  2. N’chifukwa chiyani tiyenera kukonda abale athu? (1 Yoh. 4:11, 20, 21)

  3. Kodi tingasonyeze bwanji kuti timakonda anthu anzathu? (Lev. 19:18; Aef. 5:29)

  4. Kodi tingatsanzire bwanji chikondi cha Yehova? (1 Pet. 4:8; Akol. 3:13)

  5. Kodi tingatani kuti tizitamanda Yehova? (Sal. 104:33; 146:2, 5)

  6. Kodi kukonda Yehova ndi mtima wathu wonse kumatanthauza chiyani? (Eks. 34:14; Amosi 5:15; Aroma 12:11)