Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

“Kondwerani Chifukwa cha Zimene Yehova Wachita”

“Kondwerani Chifukwa cha Zimene Yehova Wachita”

Salimo 32:11

M’MAWA

  • 9:40 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:50 Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero

  • 10:00 “Kondwerani Chifukwa cha Zimene Yehova Wachita Ndipo Sangalalani”

  • 10:15 “Okonda Dzina Lanu Adzakondwa Chifukwa cha Inu”

  • 10:30 ‘Muzidzazidwa ndi Chimwemwe’ pa Utumiki Wanu

  • 10:55 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo

  • 11:05 Musalole Kuti Mitima Yanu ‘Ilemedwe’

  • 11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:05 Nyimbo Na. 51

MASANA

  • 1:20 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:30 Nyimbo Na. 111

  • 1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu

  • 1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:15 Nkhani Yosiyirana: Yehova Ndi Amene Amatithandiza Kuti Tizikhala Osangalala

    • • Tikamathandiza Anthu Kuti Akhale Ophunzira

    • • Tikamathandiza Okhulupirira Anzathu

    • • Tikamapirira Mayesero

  • 3:00 Nyimbo Na. 2 ndi Zilengezo

  • 3:10 Muziika Yehova Patsogolo Panu Nthawi Zonse

  • 3:55 Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero