Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. 1. Kodi ndi zinthu zitatu ziti zimene Yehova amatichitira kuti tizisangalala? (Sl 32:1-10)

  2. 2. Kodi tingatani kuti tizisangalala panopa? (Sl 5:11, 12; 91:14)

  3. 3. Kodi tingatani kuti tizisangalala pa utumiki wathu ngakhale kuti tikukumana ndi mavuto? (Mac 13:50-52; Aro 5:3-5)

  4. 4. Kodi tingatani kuti tipewe ‘kulemedwa’ n’kumakhala osasangalala? (Lu 21:34)

  5. 5. Kodi Yehova amatithandiza bwanji kuti tizikhala osangalala? (Sl 92:4, 5)

  6. 6. N’chiyani chingatithandize kuti tiziika Yehova patsogolo pathu nthawi zonse? (Aro 1:20; De 6:6-9; Afi 4:6; Sl 16:3)