Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. 1. Kodi atumiki a Yehovafe tili ndi mwayi wotani? (Miy. 27:11)

  2. 2. Kodi tingatsanzire bwanji Yesu ndi kusangalatsa mtima wa Yehova? (Yoh. 8:29)

  3. 3. Kodi tingatani kuti tisangalatse mtima wa Yehova mu utumiki? (Yoh. 15:8)

  4. 4. Kodi tingatani kuti tizisangalatsa Yehova pa zochita zathu zonse? (Yoh. 14:31; Aef. 6:1-4; Sal. 35:18; 1 Pet. 2:12)

  5. 5. Kodi tingapirire bwanji mavuto, kukhumudwa komanso mayesero? (Neh. 8:10)