Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Muzisangalatsa Mtima wa Yehova!

Muzisangalatsa Mtima wa Yehova!

Miyambo 27:11

M’MAWA

  • 9:30 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:40 Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero

  • 9:50 Muzisangalatsa Mtima wa Yehova!

  • 10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzitsanzira Makhalidwe 4 a Yehova

    • • Chilungamo

    • • Kugwiritsa Ntchito Mphamvu

    • • Nzeru

    • • Chikondi

  • 11:05 Nyimbo Na. 81 ndi Zilengezo

  • 11:15 Muzilemekeza Yehova Pamene ‘Mukubala Zipatso Zambiri’

  • 11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:00 Nyimbo Na. 49

MASANA

  • 1:10 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:20 Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero

  • 1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Kodi Mungatani Kuti Muzisangalatsa Mulungu?

  • 2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:30 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo

  • 2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzisangalatsa Yehova . . .

    • • Pamoyo Wanu

    • • M’banja lanu

    • • Mumpingo Wanu

    • • M’dera Limene Mukukhala

  • 3:40 ‘Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Chingakupatseni Mphamvu’

  • 4:15 Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero