Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Musaleke Kukwaniritsa Chilamulo cha Khristu

Musaleke Kukwaniritsa Chilamulo cha Khristu

M’MAWA

  • 9:40 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:50 Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero

  • 10:00 Kodi Chilamulo cha Khristu N’chiyani?

  • 10:15 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu Ngakhale Pamene Anthu Ena Sakukuonani

  • 10:30 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu Mukamalalikira

  • 10:55 Nyimbo Na. 70 ndi Zilengezo

  • 11:05 N’chifukwa Chiyani Tingati Chilamulo cha Khristu Ndi Chabwino Kwambiri?

  • 11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:05 Nyimbo Na. 51

MASANA

  • 1:20 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:30 Nyimbo Na. 76

  • 1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu

  • 1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:15 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu M’banja Lanu

  • 2:30 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu Mukakhala Kusukulu

  • 2:45 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo

  • 2:55 Muzikondana Ngati Mmene Yesu Anakukonderani

  • 3:55 Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero