Lamlungu
“Sangalala mwa Yehova, ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako”—Salimo 37:4
M’MAWA
-
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
9:30 Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero
-
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tikhoza Kumasangalalabe Ngakhale Kuti . . .
-
• Tikukumana ndi Masautso (Aroma 5:3-5; 8:35, 37)
-
• Tikukumana ndi Zowawa (2 Akorinto 4:8; 7:5)
-
• Tikuzunzidwa (Mateyu 5:11, 12)
-
• Tikuvutika ndi Njala (Afilipi 4:11-13)
-
• Tikuvutika ndi Usiwa (1 Akorinto 4:11, 16)
-
• Tikukumana ndi Zoopsa (2 Akorinto 1:8-11)
-
• Tikuopsezedwa ndi Lupanga (2 Timoteyo 4:6-8)
-
-
11:10 Nyimbo Na. 9 ndi Zilengezo
-
11:20 NKHANI YA ONSE: Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Chuma Chomwe Sichiwonjezerapo Ululu? (Miyambo 10:22; 1 Timoteyo 6:9, 10; Chivumbulutso 21:3-5)
-
11:50 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
-
12:20 Nyimbo Na. 84 ndi Kupuma
MASANA
-
1:40 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
1:50 Nyimbo Na. 62
-
1:55 VIDIYO: Nehemiya: “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”—Mbali Yachiwiri (Nehemiya 8:1–13:30; Malaki 1:6–3:18)
-
2:40 Nyimbo Na. 71 ndi Zilengezo
-
2:50 ‘Muzisangalala Kwambiri mwa Yehova’ (Salimo 16:8, 9, 11; 37:4)
-
3:50 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza