Lachisanu
“Uthenga wabwino wa chimwemwe chachikulu chimene anthu onse adzakhale nacho”—Luka 2:10
M’mawa
8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 150 Komanso Pemphero
8:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: N’chifukwa Chiyani Tikufunikira Uthenga Wabwino? (1 Akorinto 9:16; 1 Timoteyo 1:12)
9:10 VIDIYO:
Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 1
Kuwala Kwenikweni kwa Dziko—Mbali Yoyamba (Mateyu 1:18-25; Luka 1:1-80; Yohane 1:1-5)
9:45 Nyimbo Na. 96 Komanso Zilengezo
9:55 NKHANI YOSIYIRANA: ‘Anatsogoleredwa ndi Mzimu Woyera’
• Mateyu (2 Petulo 1:21)
• Maliko (Maliko 10:21)
• Luka (Luka 1:1-4)
• Yohane (Yohane 20:31)
11:10 Nyimbo Na. 110 Komanso Kupuma
Masana
12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 117
12:50 NKHANI YOSIYIRANA: Muzikhulupirira Choonadi Chokhudza Yesu
• Mawu (Yohane 1:1; Afilipi 2:8-11)
• Dzina Lake (Machitidwe 4:12)
• Kubadwa Kwake (Mateyu 2:1, 2, 7-12, 16)
1:30 Nyimbo Na. 99 Komanso Zilengezo
1:40 NKHANI YOSIYIRANA: Zomwe Tikuphunzira pa Moyo wa M’nthawi ya Yesu
• Malo (Deuteronomo 8:7)
• Chakudya (Luka 11:3; 1 Akorinto 10:31)
• Moyo Wapakhomo (Afilipi 1:10)
• Moyo Wapamudzi (Deuteronomo 22:4)
• Maphunziro (Deuteronomo 6:6, 7)
• Kulambira (Deuteronomo 16:15, 16)
3:15 N’chifukwa Chiyani Uthenga Wabwino Umatchulidwa Kuti ndi ‘Uthenga Wosatha’? (Chivumbulutso 14:6, 7)
3:50 Nyimbo Na. 66 Komanso Pemphero Lomaliza