Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

GAWO 3

“Chikondi Chimene Khristu Ali Nacho Chimatikakamiza”

“Chikondi Chimene Khristu Ali Nacho Chimatikakamiza”

Kodi n’chiyani chimene chimatipangitsa kuti tizitsatira Yesu? Mtumwi Paulo anayankha kuti: “Chikondi chimene Khristu ali nacho chimatikakamiza.” (2 Akorinto 5:14) M’gawoli tiphunzira mmene Yesu ankakondera Yehova, anthu onse komanso munthu aliyense payekha. Tikaphunzira za chikondi chimenechi nafenso tilimbikitsidwa kuti tiziyesetsa kutsanzira Mbuye wathu.