Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

GAWO 1

“Tiye Ukaone” Khristu

“Tiye Ukaone” Khristu

Yesu anakhala ndi moyo padziko lapansili ngati munthu zaka pafupifupi 2,000 zapitazo. Komabe, n’zotheka masiku ano kuti ife ‘tione’ Mwana wa Mulungu. (Yohane 1:46) Nkhani za m’mabuku a Uthenga Wabwino zimafotokoza momveka bwino makhalidwe ake ndiponso mmene ankachitira zinthu. M’gawoli, tikambirana makhalidwe ochititsa chidwi amene Yesu ali nawo.