Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

February 8, 2000

Mmene Vuto la Mabanja Opanda Bambo Lingathetsedwere 3-11

Ana ochulukirachulukira akuleredwa popanda abambo. Kodi chikuchititsa vuto losautsali n’chiyani? Kodi mabanja angathandizidwe bwanji kuti akhalebe olimba?

3 Mabanja Opanda Bambo—Chizindikiro cha Nthaŵi

4 Chifukwa Chimene Abambo Akusoŵera

8 Mmene Vuto la Mabanja Opanda Bambo—Lingathetsedwere

12 Anthu Ovutika ndi Nkhondo Asintha

13 Kusiyana Pakati pa Olemera ndi Osauka Kukukula

22 Mliri wa Matenda a Makoswe—Unakantha Ulaya M’Nyengo Zapakati

25 Kupanga Mapu Osonyeza Miyamba—M’nthaŵi Zakale Ndiponso Tsopano

28 Lingaliro la Baibulo

Kunama—Kodi Nthaŵi Zina N’kolungama?

26 Kamzimbi—Mbalame Yokongola kwambiri

32 ‘Linandithandiza Kupenda Moyo Wanga’

Kodi Ndingapeŵe Bwanji Zoopsa pa Intaneti? 19

Achinyamata ambiri akugwiritsa ntchito Intaneti. Kodi ndi motani mmene angagwiritsire ntchito mwanzeru chida champhamvu chimenechi?

Kumeta Moyeretsa 22

Tsiku ndi tsiku amuna padziko lonse amameta ndevu zawo. Kodi mbiri yometa ndevu ili yotani? Ndipo kodi mungamete bwanji moyeretsa?