Zamkatimu
Zamkatimu
August 8, 2000
Kodi Kukhulupirira Mizimu N’kothandiza Kapena N’kovulaza?
Kodi n’chifukwa chiyani anthu ambiri padziko lonse ayamba kukhulupirira mizimu? Kodi kukhulupirira mizimu n’koopsa? Ngati kuli koopsa, kodi mungadziteteze bwanji?
3 N’chifukwa Chiyani Kukonda Kukhulupirira Mizimu Kwafala Motere?
4 Chifukwa Chimene Muyenera Kupeŵera Kukhulupirira Mizimu
9 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
Kodi Ndingakhale Wopambana Motani Pamene Ndikukhala Kudziko Lina?
12 Kodi Ufulu Wokulirapo wa Chikumbumtima Udzaperekedwa M’Mexico?
14 Kodi Chisoni Chiyenera Kusonyezedwa?
Kudzikongoletsa—Kufunika kwa Kusamala
18 Kugwiritsa Ntchito Wailesi ya Kanema Mosamala Kwambiri
19 Kusagwirizana ndi Mankhwala Osiyanasiyana Matenda Ovuta Kuwamvetsa
20 Mukadwala Chifukwa cha Mankhwala
24 Kuthandiza Anthu Odwala MCS
31 Mtundu Wodabwitsa wa Mbalame
32 Kulera Ana Ophunzitsika Bwino—Motani?
Kodi Mankhwala Ogwiritsidwa Ntchito Tsiku N’tsiku—Akukudwalitsani? 19-26
Anthu ambiri amadwala chifukwa cha mankhwala amene amaikidwa m’zinthu zogwiritsidwa ntchito panyumba tsiku n’tsiku kapenanso m’zinthu zina. Kodi pali chithandizo chotani kwa anthu otere?