Zamkatimu
Zamkatimu
October 8, 2000
Thambo—Kodi Linakhalako Mwamwayi?
Thambo lathu lili ndi zinthu zosaŵerengeka. Kodi zinakhalapo bwanji? Kodi umboni wasayansi umasonyeza chiyani?
3 Thambo Lathu Lodabwitsali—Kodi Linangokhalako Mwamwayi?
5 Kodi Maelementi Anakhalako Mwamwayi?
8 Dziko Lapansi—Kodi “Maziko” Ake Anakhalako Mwamwayi?
15 Nyamalikiti—Nyama Zamisinkhu Yaitali, Zamiyendo Yaitali, Ndiponso Zokongola
19 Kukhalabe Okhulupirika mu Ulamuliro Wankhanza
23 Kodi “Ntchito Yokhazikika” Idamka Kuti?
28 Chimene Ndimaikirapo Mtima Kwambiri Ndicho Kukhalabe Wokhulupirika
N’chifukwa Chiyani Ndili Wochepa Thupi Chonchi? 12
Achinyamata ena amadziona ngati osaoneka bwino chifukwa chakuti n’ngochepa thupi. Onani malingaliro anzeru amene angathandize achinyamata kuthana ndi vutoli.
“Maseŵera Angozi”—Kodi Muyenera Kuika Moyo Wanu Pachiswe Mwakuwachita? 26
Kodi Baibulo limati chiyani pankhani imeneyi?
[Chithunzi pachikuto]
Chikuto: Gulu lozungulira la nyenyezi lotchedwa NGC 5236
[Mawu a Chithunzi]
Mwachilolezo cha Anglo-Australian Observatory, chithunzi anajambula ndi David Malin
[Chithunzi patsamba 2]
Tsamba 2: Magulu aŵiri ozungulira a nyenyezi akudutsana
[Mawu a Chithunzi]
NASA ndi The Hubble Heritage Team (STScI)