Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

July 8, 2001

Vuto La Mankhwala Osokoneza Bongo Lingathetsedwe!

Kodi kwenikweni mankhwala oopsa ndi ati? N’chifukwa chiyani anthu amalephera kusiya kuwagwiritsa ntchito? Kodi vutoli lingatheretu?

3 Kodi Ndani Amagwiritsa Ntchito Mankhwala Osokoneza Bongo?

6 N’chifukwa Chiyani Anthu Amagwiritsa Ntchito Mankhwala Osokoneza Bongo?

9 Vuto la Mankhwala Osokoneza Bongo Lingathetsedwe!

19 Kodi Padzikoli Madzi Akutha?

22 Kodi Madzi Onse Aja Amka Kuti?

26 Kufufuza Madzi Amoyo

30 Lingaliro Labaibulo

Kodi Kulira Maliro N’kulakwa?

32 Lingakuthandizeni Wokondedwa Wanu Akamwalira

Kodi Mulungu Angamve Mapemphero Anga? 12

Kodi mungakhale bwanji otsimikiza kuti Mulungu angamve mapemphero anu? Kodi mungatani kuti Mulungu afike pokhala mnzanu?

Dera la Maluŵa Okongola Koposa 15

Dera lotchedwa Fynbos ku South Africa lili ndi mitundu yazomera yochuluka zedi imene siipezekanso kwina kulikonse padziko.