Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

September 8, 2001

Kuthandiza Achinyamata Amene Akuvutika Maganizo

Zikuoneka kuti achinyamata akuvutika maganizo kwambiri kuposa kale lonse. N’chifukwa chiyani zili choncho? Kodi angathandizidwe bwanji?

3 Msinkhu Umene Uli Patsoka Lalikulu

5 Kudziŵa Zizindikiro Zake

8 Kudziŵa Zoyambitsa Zake

10 Mmene Mungathandizire

15 Anthu Akuona Ukalamba Mosiyana ndi Kale

19 Pamene Mwakumana ndi Zoopsa

20 Kodi Vuto Lokhala Wamantha Mukamakumbukira Zoopsa Ndi Lotani Kwenikweni?

23 Vuto la Mantha Lidzatha!

32 Vuto Losamalira Ana

Kodi Ndingatani Kuti Kuŵerenga Baibulo Kuzindisangalatsa? 27

Achinyamata ena anayamba kukonda kuŵerenga Baibulo. Lingalirani zinthu zimene zingachititse kuti kuŵerenga Baibulo kuzikusangalatsani.

Kodi Mulungu Ankakondwera ndi Malonda a Ukapolo? 30

Ukapolo wapangitsa anthu ambirimbiri kuvutika moipa zedi. Kodi Mulungu amavomereza kuzunza anthu moipa choncho?