Zisonyezero za Voliyumu 83 ya Galamukani!
Zisonyezero za Voliyumu 83 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Anthu Okhala M’chipinda Chimodzi, 5/8, 6/8, 7/8
Khalidwe la Anzanga, 12/8,
Kodi Mukufunika Telefoni ya M’manja? 11/8
Kodi N’Chifukwa Chiyani Kholo Langa Silindikonda? 10/8
Kodi Pali Vuto Lotani Ndi Zamatsenga? 2/8
Kukhala N’chibwenzi, 1/8
Kukhala Wokongola, 8/8
Kulalikira Anzanu Akusukulu? 3/8, 4/8
Opaleshoni Yodzikongoletsa, 9/8
CHIPEMBEDZO
Kodi Mdyerekezi Alikodi? 3/8
“Kupemphera Pawekha,” 5/8
Mapemphero Opempha Mtendere, 11/8
CHUMA NDI NTCHITO
Aphunzitsi, 3/8
Kumalo Antchito Nkotetezeka Bwanji? 3/8
Malingaliro Oyenera a Ntchito, 3/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Chikondwerero cha Chaka Chatsopano, 1/8
Khirisimasi, 12/8
Kodi Akristu Ayenera Kulalikira? 6/8
Kodi Mulungu Amanyalanyaza Zofooka? 11/8
Kodi Mulungu Amavomereza Nkhondo? 5/8
Kudziona Ngati Wolakwa, 3/8
Kutetezedwa ndi Mulungu, 4/8
Maphempero Amene Mulungu Amamva, 9/8
Mikaeli Mngelo Wamkulu, 2/8
Mmene Mulungu Amachionera Chiwawa, 8/8
Zinthu Zakale Zofukulidwa Pansi, 10/8
Zithunzi Zolaula, 7/8
MAUNANSI A ANTHU
Amayi, 4/8
Kulimbikitsa Amene Akulira Maliro, 5/8
Mabanja Akholo Limodzi, 10/8
Tsiku Laukwati, 2/8
Ukwati Ndiwo Mgwirizano Wosatha, 2/8
MAYIKO NDI ANTHU
Amasai—Anthu Odabwitsa Ndiponso Ochititsa Kaso, 3/8
Kupulumuka Zoopsa Phiri Litaphulika N’kumatuluka Chiphalaphala (Congo [Kinshasa]), 11/8
MBONI ZA YEHOVA
Kugwiritsa Ntchito Galamukani! Mwanjira Yabwino, 9/8
Kuthandiza Anthu Amene Tsoka Lalikulu Linawagwera (Texas, U.S.A.), 12/8
Kutsutsana Pankhani Anaonetsa pa TV (Georgia), 8/8
Misonkhano Yachigawo ya “Olengeza Ufumu Achangu,” 6/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Kudalira Mulungu Kunandilimbitsa (R. Sacksioni-Levee), 1/8
Kukumananso Modabwitsa (D. Sheets, M. Ruge), 11/8
Wandale Anasanduka Mkristu Wosakhudzidwa N’zandale (L. Šmejkal), 7/8
SAYANSI
Kodi Sayansi ndi Chipembedzo Zingagwirizane? 6/8
Mdima Ukagwa Masana (Kadamsana), 9/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Achinyamata Ovutika ndi Tulo, 8/8
Chakudya Chopatsa Thanzi, 5/8
Chakudya Chosakayikitsa, 1/8
Dzitetezeni Kuti Musagonthe M’kutu! 6/8
Edzi, 11/8
Matenda a Kuthamanga kwa Magazi, 5/8
Ndinapita Padera, 4/8
Uchi—Mankhwala Ozuna, 3/8
Vuto la Kusokonezeka Maganizo Atabereka, 8/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Chakumwa Chochokera ku Chitsamba Chachilendo, 5/8
Chinenero cha Kutchire—Kulankhulana kwa Zinyama, 4/8
Mbidzi, 2/8
Tizilombo Tochotsa Nyansi, 6/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Kodi Apolisi Ndi Ofunika Chifukwa Chiyani? 7/8
Kodi Kuyenda Pandege N’kwabwinobe? 12/8
Kodi Nzongopeka Kuti Dziko Lonse Lidzakhala Pamtendere? 5/8
Kudalirana kwa Mayiko, 6/8
Kuphunzirapo Kanthu Pazochitika Zakumbuyoku, 8/8
Kutchova Njuga, 8/8
Mabanja Akholo Limodzi, 10/8
Opulumuka Chivomezi, 4/8
Othawa Kwawo, 2/8
Tsiku Limene Nyumba Zosanja Ziŵiri Zinagwa, 1/8
Ukapolo, 7/8
Zida Zofalitsa Tizilombo Topereka Matenda, 10/8
Zinyalala, 9/8
ZOSIYANASIYANA
Anthu Okonda Zinthu Zonyamula Mtima, 10/8
Kodi Anali Munthu Wolimbikitsa Nkhondo? (Alfred B. Nobel), 5/8
Manambala (Zokhulupirira Manambala), 9/8
Ngozi Zapamsewu, 9/8
Zombo Zamphamvu (zoswa ayezi), 12/8