Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Moyo Ndi Wamtengo Wapatali

Moyo Ndi Wamtengo Wapatali

Moyo Ndi Wamtengo Wapatali

Moyo ndi mphatso ya mtengo wapatali imene tiyenera kuiyamikira. Koma n’chifukwa chiyani nthaŵi zambiri timavutika? Kodi Mulungu amatisamaliradi? Mafunso amenewa akuyankhidwa mu kabuku kamasamba 32 kamene akasonyeza pansipa.

□ Nditumizireni kabuku ka mutu wakuti Kodi Mulungu Amatisamaliradi?

□ Chonde nditumizireni munthu kuti ayambe kuchita nane phunziro la Baibulo lapanyumba laulere.

[Mawu a Chithunzi patsamba 32]

Kagalu: Courtesy of The Pedigree Mutt Pet Shop