Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

April 8, 2003

Mungatani Ngati Mwana Wanu Anayamba Mankhwala Osokoneza Bongo?

Achinyamata ambiri padziko lonse ayamba mankhwala osokoneza bongo. Kodi makolo angawathandize motani ana awo?

3 Mankhwala Osokoneza Bongo Pakati pa Achinyamata

5 Mmene Mungatetezere Ana Anu

10 Vuto la Mankhwalaŵa Litha Posachedwapa Padziko Lonse

11 Kodi Kugona N’kofunikadi Kapena Sikofunika Kwenikweni?

14 Zimene Mungachite Kuti Muzigona Bwino

23 Kudya Opanda Mafoloko ndi Mipeni

26 Ulendo Wokaona Munda wa Nthochi

29 Miyambi ya Aakani Imasonyeza Chikhalidwe Chawo

32 Msonkhano Wofunika Kwambiri Pachaka

Kodi Kukonda Chuma N’kutani Makamaka? 18

Kodi Baibulo limatipo chiyani pankhani ya kukhala ndi chuma?

Kodi Ndizisankha Motani Matepi a Nyimbo Oti Ndizionera? 20

Achinyamata ambiri amakonda kuonera matepi a nyimbo. Kodi ndi mfundo za m’Baibulo ziti zimene zingakuthandizeni kusankha nyimbo zabwino zoti muzionera?