Zisonyezero za Voliyumu 84 ya Galamukani!
Zisonyezero za Voliyumu 84 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Kuonera Matepi a Nyimbo: 3/8; 4/8
Kuonera M’kalasi: 2/8
Kutengeka N’zochita za Anzanga: 1/8
Kuyesa Kumangochita Chilichonse Mosalakwitsa?: 8/8; 9/8
Mwana wa Makolo Amene Sanandibereke: 5/8; 6/8
Ndilembe Chizindikiro pa Thupi Langa?: 10/8
Ndingatani Kuti Anthu Asamangofanizira Zochita Zanga ndi za Makolo Anga?: 11/8
Ndingatani Kuti Anthu Asamangofanizira Zochita Zanga ndi za Mbale Wanga?: 12/8
Tsoka Likandigwera: 7/8
CHIPEMBEDZO
LINGALIRO LA BAIBULO
Akristu Amafunika Kuti Azikhala Osauka?: 1/8
Akristu Azichita Zogodomalitsa Maganizo?: 7/8
Kudana ndi Anthu Amitundu ina N’koyenera?: 8/8
Kukonda Chuma N’kutani Makamaka?: 4/8
Makhalidwe a Kugonana Kwachilendo: 10/8
Mulungu Amatidalitsa ndi Chuma?: 9/8 1
Okondedwa Anu Akakhala Achikhulupiriro China: 11/8
Peŵani Mawu Opweteka: 6/8
Tchimo Limene Silingakhululukidwe: 2/8
Tingalimbane Bwanji ndi Zilakolako Zoipa?: 12/8
Ufulu Wosankha?: 3/8
Umodzi wa Akristu Umalira Kuchita Chilichonse Mofanana?: 5/8
MAUNANSI A ANTHU
Kulankhulana: 10/8
Kupezerera Ena: 9/8
Mwana Wanu Anayamba Mankhwala Osokoneza Bongo: 4/8
Ubwana: 5/8
MAYIKO NDI ANTHU
Kudya Opanda Mafoloko ndi Mipeni (Ghana): 4/8
Miyambi ya Aakani (Ghana): 4/8
Nkhalango ya Nairobi (Kenya): 6/8
St. Petersburg (Russia): 9/8
Syria: 2/8
MBONI ZA YEHOVA
Chikondi Panthaŵi ya Mavuto (Nigeria): 3/8
Chimene Mkuntho Sunathe Kukokolola (ntchito yothandiza): 8/8
Khoti Lalikulu ku America Ligamula za Ufulu Woyankhula: 1/8
Nkhani Yochititsadi Chidwi (mwana wa sukulu): 9/8
Zitaphulika (Ecuador): 9/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Chiyambi cha Moyo Wokhutiritsa (E. Pandachuk): 11/8
Kusiya Ntchito Yopha Anthu N’kuyamba Yolimbikitsa Mtendere (T. Niwa): 3/8
Kuvutikira Chikhulupiriro ku Slovakia (J. Bali): 1/8
Kuvutikira Chikhulupiriro ku Ulaya mu Ulamuliro wa Nazi (A. Letonja): 2/8
Mmene Moyo Wanga Unasinthira N’tachita Ngozi (S. Ombeva): 5/8
Ndinaphera Ludzu la Mawu a Mulungu (L. Moussanett): 7/8
Ndinasiya Khalidwe Lokakala Mtima (J. Gomez): 1/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Kamtengo Kamene Kamayeretsa Mano: 9/8
Kugona: 4/8
Kusoŵa Zakudya M’thupi: 3/8
Madzi: 7/8
Majeremusi Osamva Mankhwala: 11/8
Matenda a Shuga: 5/8
Matenda Ofalitsidwa Ndi Tizilombo: 6/8
Mmene Mungatetezere Pathupi: 1/8
Muzigona Mokwanira!: 2/8
Mwana Akatentha Thupi: 12/8
Njira Zisanu ndi Imodzi Zosamalira Thanzi Lanu: 10/8
Sopo Ndi “Katemera Amene Mungadzipatse Nokha”: 12/8
Zimene Mumasankha Zimakhudza Thanzi: 9/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Chakudya Chochokera M’dimba Lanu: 12/8
Kulankhulana: 10/8
Maso a Chiwombankhanga: 1/8
Mbalame Zofiira Nthenga, Zodziŵa Kuvina (flamingos): 2/8
Msamuko Waukulu Wochititsa Chidwi (nyumbu): 3/8
Munda wa Nthochi: 4/8
Mvuu: 5/8
Nkhalango ya Nairobi: 6/8
Nkhalango za M’madera Otentha: 7/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Chiwawa Choopsa: 7/8
Kupezerera Ena: 9/8
Kusoŵa Zakudya M’thupi: 3/8
Mafuta—Kodi Adzatha?: 11/8
Mfundo Zabwino za Moyo: 6/8
Misonkho Ndi Yokwera Kwambiri?: 12/8
Mwana Wanu Anayamba Mankhwala Osokoneza Bongo: 4/8
Nyengo: 8/8
Titeteze Zinthu Zachilengedwe?: 12/8
Uhule wa Ana: 2/8
Ulimi Sukuyenda Bwino?: 10/8
Zithunzi Zolaula: 8/8
ZOSIYANASIYANA
Anthu Amatengera Mmene Mlengi Analengera Zinthu (magolobo): 12/08
Galimoto, Zamakedzana ndi Zamakono: 1/8
Kumwetulira: 2/8
Mafashoni: 9/8
‘Musaiwale Ambulera!’: 8/8
Nsapato Zimakukwanani Bwinobwino?: 3/8
Osamangokhulupirira za M’maluŵa (Intaneti): 2/8