Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

January 8, 2004

Kumvetsetsa Matenda A Maganizo

Padziko lonse, matenda a maganizo ochititsa munthu kungokhala woipidwa ndiponso ochititsa munthu kusinthasintha zochitika amasautsa amuna ndi akazi ambimbiri. Kodi odwala matendaŵa angathandizidwe bwanji?

3 Anthu Osautsika Maganizo

4 Kukhala ndi Matenda a Maganizo

8 Nkhani Yabwino kwa Odwala Matendaŵa

12 Mmene Ena Angathandizire

16 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .

Kodi Ndingathe Bwanji Kukamba Nkhani Bwino Pagulu?

19 Kubadwira M’dziko Lopanda Chikondi!

20 Zimene Makanda Amafunikira Ndiponso Zimene Amafuna

24 Kupatsa Ana Zimene Amafunikira

31 Zomera N’zothandiza Kwambiri Popanga Mankhwala

32 Kukhalabe Osangalala Ngakhale M’mavuto

Kodi Zokambirana za Mayiko Zidzabweretsa Mtendere Padziko Lonse? 14

N’chifukwa chiyani anthu akamayesa kukambirana zamtendere kaŵirikaŵiri siziphula kanthu?

Kodi Mankhwala Ochokera ku Zitsamba Angakuthandizeni? 28

Mankhwala ochokera ku zitsamba ayamba kutchuka kwambiri. Koma kodi ndi zinthu zotani zimene n’kwanzeru kusamala nazo?