Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

April 8, 2004

Kodi Dzikoli Lingasinthidwe Kuti Likhale Labwino?

Anthu ambiri amaona kuti zinthu zambiri padziko pano, kuphatikizapo moyo wa anthu n’zofunika zitasintha kwabasi. Koma kodi akuluakulu ofuna kusintha zinthu angakwanitse kutero? Ngati iwoŵa sangatero, ndani amene angakwanitse?

3 Kufunitsitsa Kusintha Zinthu

5 Kodi Anthu Ofuna Kusintha Zinthu Angakwanitse Kutero?

11 Chinthu Chabwino Koposa Kusintha Kotereku

18 Anapulumuka Madzi Atasefukira!

19 Kusamvana Pankhani ya Mose

20 Kodi Mose Anali Munthu Weniweni Kapena Wongopeka?

26 Mmene Moyo wa Mose Umakukhudzirani

30 Lingaliro la Baibulo

Kodi n’zotheka Kusiya Zizoloŵezi Zoipa?

32 Tsiku Lofunika Kulikumbukira Lamlungu pa April 4, 2004

N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Tizivutika? 12

Kodi tiyenera kumupsera mtima Mulungu chifukwa cholola kuti tizivutika? Onani yankho logwira mtima la funsoli lomwe lili m’Baibulo.

Sungani Nthaŵi! 15

Vuto la kuchedwa lingasokoneze kwambiri moyo ndiponso ntchito ya munthu. Naŵa malangizo ena amene angakuthandizeni kusunga nthaŵi.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

COVER: Globe: Used with permission from The George F. Cram Company, Indianapolis, Indiana

UN/DPI Photo by Eskinder Debebe