Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

June 8, 2004

Kukhala Nokhanokha Koma Osasungulumwa

N’chifukwa chiyani anthu ambiri ali osungulumwa? Kodi munthu angachite chiyani kuti athane ndi kusungulumwa? Kodi padzakhala nthaŵi imene sipadzakhalanso munthu wosungulumwa?

3 N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Ali Osungulumwa?

5 Kuthana ndi Kusungulumwa

9 Nthaŵi Imene Sipadzakhalanso Munthu Wosungulumwa

18 N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Amadwala Chimfine Chimene Chimabwera Akakhala Pafupi ndi Mungu?

19 Nkhondo Yakalekale Yofuna Kupeza Thanzi Labwino

23 Kupambana ndi Kulephera pa Nkhondo Yolimbana ndi Matenda

27 Dziko Lopanda Matenda

30 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .

N’chifukwa Chiyani Chibwenzi Changa Chimandizunza Chonchi?

Matayala Angapulumutse Moyo Wanu 12

Matayala abwino ndi ofunika kwambiri kuti galimoto isachite ngozi. Kodi mungawasamale bwanji?

Kodi Kuda Nkhaŵa N’kupanda Chikhulupiriro? 16

Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani imeneyi?