Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

January 8, 2005

Kodi Dziko Lathuli Lipulumuka?

Zinthu zachilengedwe za padziko pano zikutha modetsa nkhawa. Kodi ndani angathetse vutoli?

3 Dziko Lathuli Likusakazidwa Kwabasi

4 Zinthu Zachilengedwe Zikutha Padziko Pano

10 Dziko Lathuli Lidzapulumuka

15 Ulendo Wosaiwalika Wokaona Chigwa cha Ngorongoro

18 “Ndikanakonda Anthu Akanadziwa Zimenezi!”

19 Kunyanyira Kufuna Kukongola

20 Kuipa Kofunitsitsa Kukhala Wokongola

24 Kukongola Kofunika Kwambiri

26 Kwalembedwa Kuti Ndidzawaonanso

Kodi Ndingatani Mnyamata Amene Ndimamufuna Akandikana? 12

Kodi mtsikana angatani mnyamata amene amamufuna akamukana?

Kodi Kufatsa N’kupanda Mphamvu? 31

Anthu ambiri masiku ano angayankhe kuti inde n’kupanda mphamvu, koma Baibulo limasonyeza kuti si choncho ayi.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

COVER: NASA JSC