Zamkatimu
Zamkatimu
February 8, 2005
Zimene Mungachite Kuti Moyo Wanu Usakhale Wopanikizika
Akatswiri ambiri akukhulupirira kuti kukhala ndi moyo wopanikizika kungawononge kwambiri thanzi la munthu. Kodi zinthu zina zimene zimachititsa moyo kukhala wopanikizika masiku ano n’ziti? Werengani nkhani zofotokoza zinthu zina zomwe mungachite kuti muchepetse kupanikizika pamoyo wanu.
3 Kusowa Mtendere Chifukwa cha Moyo Wopanikizika
4 Zimene Zimachititsa Moyo Kukhala Wopanikizika ndi Zotsatirapo Zake
7 Pali Zimene Mungachite Kuti Moyo Wanu Usakhale Wopanikizika
17 Zimene Zikuchitikira Madokotala M’dziko Limene Likusinthali
19 Madokotala Amakumana N’zambiri
22 Kodi Udokotala uli ndi Tsogolo Lotani?
26 Kodi Mafoni A M’manja ndi Abwino Kapena ndi Oipa?
29 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
Kodi Ndiyenera Kutani Anthu Ena Akandiuza Mavuto Awo?
32 Buku la Achinyamata Limene Ambiri Amaliyamikira
Kupatsa Ana Chisamaliro Chimene Amafunikira 12
Kodi makolo ayenera kuchita chiyani kuti apatse ana awo chisamaliro chimene amafunikira?
“Ndinu Dr. Livingstone, Eti?” 14
Kukumana kwa Stanley ndi Livingstone kunali kochititsa chidwi kwambiri, komanso kunali kothandiza m’njira zina. Onani zifukwa zomwe ntchito ya amuna awiri amenewa yakhudzira kwambiri miyoyo ya anthu ochuluka.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
From the book Missionary Travels and Researches in South Africa, 1858