Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

June 8, 2005

Mmene Mungadzitetezere ku Khansa Yapakhungu

Tiyenera kuteteza khungu lathu kuti lisapse ndi dzuwa, chifukwa likhoza kuwonongeka.

3 Maganizo a Anthu Asintha pa Nkhani ya Khungu Ayamba Kufuna Khungu Loderako Osati Loyera

4 Tetezani Khungu Lanu

9 Kupirira ndi Khansa Yapakhungu

11 “Muzinyadira Zimenezi”

14 Dzitetezeni Kuti Musafe ndi Utsi

15 Zomwe Tonsefe Tingachite Kuti Pakhomo Pazikhala Paukhondo

19 Kodi Mumafunikadi Kuchita Zinthu Zolimbitsa Thupi?

23 Kodi Mumachita Mokwanira Zinthu Zolimbitsa Thupi?

31 Kodi Dzuwa Lingawale Bwanji Pakati pa Usiku?

32 Kodi Mwakonzeka Kukapezekako?

Kodi Kufuna Kutchuka N’kulakwa? 12

Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani imeneyi?

Kodi Kupeza Chibwenzi pa Intaneti Kungakhaledi Koopsa? 28

Anthu ambiri akupeza zibwenzi pa Intaneti, koma kodi imeneyi ndi njira yopanda vuto lililonse yopezera munthu woti mudzakwatirane naye?